Timu ya FCB Nyasa Big Bullets yagonjetsa timu ya Creck Sporting 4-1 kutola ma points onse atatu lero m'masewelo a mu 2025 TNM Super League omwe anachitikira pa bwalo la Kamuzu mu mzinda wa Blantyre. Zigoli ziwiri mchigawo choyamba kuchokera kwa Wongani Lungu pa mphindi ya chi 19 ndi Babatunde Adepoju pa mphindi ya 40 […]
The post FCB Nyasa Big Bullets yawaza Creck Sporting mwankhanza appeared first on Malawi 24.