Mtsogoleri wa dziko la Malawi, Lazarus Chakwera, wakanika kutsatira malamulo pamene mpaka pano sanasakhebe wachiwiri wake. Kutsatira imfa ya wakale wachiwiri kwa pulezidenti Dr. Saulos Chilima yemwe analowa mmanda pa 17 June, Bungwe loyendetsa malamulo m'dziko muno linauza Chakwera kuti akuyeneka kusakha omutsatira watsopano pasanapitilire pa 19 June. Anthu ambiri m'dziko muno dzulo, tsiku loyikikali, […]
The post Chakwera akanika kutsata lamulo, sanasankhebe wachiwiri wake appeared first on Malawi 24.