Bwalo la milandu mu mzinda wa Lilongwe lagamula kuti azibambo anayi akakhale ku ndende zaka za pakati pa 13 ndi 20 kamba kotchola nyumba ina ku Area 49 komwenso adakhapako anthu, kuphatikiza ana awiri. Mneneri wa polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu wati anthuwa anali mugulu loposa anthu khumi lomwe lidakaba ku nyumbayo cha m'ma […]
The post Azibambo anayi akasewenza kundende kamba kokuba appeared first on Malawi 24.