Apolisi awotcha chamba chokwana matani awiri chomwe akhala akulanda m'boma la Salima. A Rabecca Ndiwate omwe ndi mneneri wa a polisi m'bomali ati chamba chomwe chatenthedwachi ndi chomwe eni ake adathawa ndipo sakudziwika. Mneneriyu wati apolisi apitiliza kuonetsetsa kuti m'bomali muli chitetezo chokhwima pofuna kuthana ndi mchitidwe wogula komanso kugulitsa mankhwala ozunguza bongo mwachinyengo. A […]
The post Apolisi m'boma la Salima awotcha chamba chochuluka appeared first on Malawi 24.