Pomwe mabanja ena akusowa ana palinso mabanja ena akuthawa udindo wao wopereka chisamaliro kwa ana awo obereka okha mdziko muno. Ana awiri, Loveness ndi Liviness Weremu omwe ndi amapasa azaka 13, m'mudzi mwa Jolichi mfumu yaikulu Mchilamwera ku Thyolo akulera abale awo anayi popeza makolo awo adawathawa. Loveness ndi Liviness adasiya sukulu mu sitandade 3 […]
The post Ana asanu ndi m'modzi osakwana zaka 14 ku Thyolo akulelana okhaokha appeared first on Malawi24.