Chipani chotsutsa boma cha Democratic Progressive (DPP) chatsimikiza za kutuluka m’chipani kwa a Dalitso Kabambe, koma chati sichikudandaula ponena kuti ngakhale banja limene limatha ndipo aliyese amalowera kwake. Potsatira kalata yomwe a Kabambe omwe anakhalaposo gavanala wa banki ya ikulu ya Reserve atulutsa Lolemba yolengeza za kutuluka m’chipanichi, DPP yalemba pa tsamba lake la fesibuku […]
The post Aliyese ali ndi ufulu osintha chipani – yatelo DPP appeared first on Malawi 24.