Mtsogoleri wa mbali ya otsutsa boma ku nyumba ya Malamulo muno mu Malawi a Kondwani Nankhumwa asankha phungu wa Nyumba ya Malamulo wa ku dela la Mangochi Monkey-bay a Raph Jooma kukhala owayankhulira. Malingana ndi chikalata chomwe chatuluka lero pa 28 December 2023 ndipo chasainidwa ndi ndi Mlembi wawo wamkulu a Dorothy Kabango ati ntchito […]
The post A Nankhumwa asankha Mneneli wawo appeared first on Malawi 24.