Zoti mayiko ena akaona wapolisi amaona mfuti, kapena anthu okhazikitsa chitetezo ndi zakomweko. Kuno akuti timakhala taona ngwazi za katangale. Kafukufuku amene bungwe la Afrobarometer wachita, watsimikiza kuti unyinji wa a Malawi ulibe chikhulupililo mu polisi yathu. Malinga ndi kafukufuku uyu, a Malawi ochuluka kwambili akuona ngati a polisi ochuluka ngakhale onse amene ali ndi […]
The post A Malawi akaona wapolisi amaona katangale - waulula kafukufuku appeared first on Malawi 24.