Akatswiri pa ndale ati zomwe achita a chakwera ndi kuphwanya pangano limene anapangana ndi a Malawi kuti iwo ndi nduna zawo sakhalaso ndi ulendo opita kunja kwa dziko lino pokhapokha chuma chitabwezeretsedwa mchimake dziko muno. Mu November chaka chatha, a Chakwera ananena kuti sayendanso pa ulendo otuluka m'dziko muno kufikira ku mapeto kwa March, 2024. […]
The post A Chakwera aphwanya pangano, akatswiri atero appeared first on Malawi 24.