Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Michael Usi wati iye anasankhidwa pa udindo wake ndi mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera chifukwa choti iye ndi namatetule pankhani yopemphetsa kwa azungu. A Usi ayankhula izi ku mayambiliro a sabata ino ku Ndirande munzinda wa Blantyre pomwe amamalizitsa maulendo awo ochezera anthu m'misika yosiyanasiyana mchigawo cha kummwera. […]
The post Chakwera anandisankha chifukwa ndimatha kupempha – watelo Usi appeared first on Malawi 24.