Mapemphero anasokonekera dzulo pa mpingo wa Headstone Prophetic Ministry International ku Chileka mu mzinda wa Blantyre pamene anthu omwe akuwaganizira kuti ndi a gulewamkulu atentha tchalitchi. Malingana ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Chileka a Sergeant Jonathan Phillipo, nkhaniyi yachitika mmawa wa Lamulungu pa 17 October pomwe anthu okwiyawa anakhamukira ku tchalitchichi chomwe amatsogolera ndi […]
The post Anthu okwiya atentha tchalichi appeared first on Malawi 24.